Mateyu 26:62 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 62 Atamva zimenezo mkulu wa ansembe anaimirira nʼkumufunsa kuti: “Kodi suyankha? Kodi sukumva zimene anthuwa akukunenezazi?”+
62 Atamva zimenezo mkulu wa ansembe anaimirira nʼkumufunsa kuti: “Kodi suyankha? Kodi sukumva zimene anthuwa akukunenezazi?”+