Machitidwe 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mulungu wa Abulahamu, wa Isaki ndi wa Yakobo,+ Mulungu wa makolo athu, ndi amene walemekeza Mtumiki wake+ Yesu,+ amene inu munamupereka+ ndiponso kumukana pamaso pa Pilato, ngakhale kuti Pilatoyo ankafuna kumumasula. Machitidwe 13:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ngakhale kuti sanapeze chifukwa chomuphera,+ anaumiriza Pilato kuti ameneyu aphedwe.+
13 Mulungu wa Abulahamu, wa Isaki ndi wa Yakobo,+ Mulungu wa makolo athu, ndi amene walemekeza Mtumiki wake+ Yesu,+ amene inu munamupereka+ ndiponso kumukana pamaso pa Pilato, ngakhale kuti Pilatoyo ankafuna kumumasula.