Mateyu 5:10, 11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Osangalala ndi anthu amene azunzidwa chifukwa cha chilungamo+ chifukwa Ufumu wakumwamba ndi wawo. 11 Ndinu osangalala pamene anthu akukunyozani,+ kukuzunzani komanso kukunamizirani+ zoipa zilizonse chifukwa cha ine.+ Yohane 17:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Iwo ndawapatsa mawu anu, koma dziko likudana nawo chifukwa sali mbali ya dziko,+ mofanana ndi ine amene sindili mbali ya dziko. 1 Petulo 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma ngakhale mutavutika chifukwa chochita zinthu mwachilungamo, mumakhalabe osangalala.+ Musamaope zimene amaopa* ndipo musamade nazo nkhawa.+
10 Osangalala ndi anthu amene azunzidwa chifukwa cha chilungamo+ chifukwa Ufumu wakumwamba ndi wawo. 11 Ndinu osangalala pamene anthu akukunyozani,+ kukuzunzani komanso kukunamizirani+ zoipa zilizonse chifukwa cha ine.+
14 Iwo ndawapatsa mawu anu, koma dziko likudana nawo chifukwa sali mbali ya dziko,+ mofanana ndi ine amene sindili mbali ya dziko.
14 Koma ngakhale mutavutika chifukwa chochita zinthu mwachilungamo, mumakhalabe osangalala.+ Musamaope zimene amaopa* ndipo musamade nazo nkhawa.+