Mateyu 5:39, 40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Koma ine ndikukuuzani kuti: Musamalimbane ndi munthu woipa, koma wina akakumenyani mbama patsaya lakumanja, muzimupatsanso tsaya linalo.+ 40 Ngati munthu akufuna kukutengera kukhoti kuti akulande malaya ako amkati, uzimupatsanso akunja.+ 1 Akorinto 6:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kunena zoona, ngati mukutengerana kukhoti ndiye mwalepheratu. Bwanji osangolola kulakwiridwa?+ Bwanji osalola kuberedwa?
39 Koma ine ndikukuuzani kuti: Musamalimbane ndi munthu woipa, koma wina akakumenyani mbama patsaya lakumanja, muzimupatsanso tsaya linalo.+ 40 Ngati munthu akufuna kukutengera kukhoti kuti akulande malaya ako amkati, uzimupatsanso akunja.+
7 Kunena zoona, ngati mukutengerana kukhoti ndiye mwalepheratu. Bwanji osangolola kulakwiridwa?+ Bwanji osalola kuberedwa?