Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Luka 22:46
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 46 Iye anawauza kuti: “Nʼchifukwa chiyani mukugona? Dzukani ndipo mupitirize kupemphera kuti musalowe mʼmayesero.”+

  • 1 Akorinto 10:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Palibe mayesero amene mwakumana nawo osiyana ndi amene anthu ena amakumana nawo.+ Koma Mulungu ndi wokhulupirika ndipo sadzalola kuti muyesedwe kufika pamene simungapirire,+ koma pamene mukukumana ndi mayeserowo iye adzapereka njira yopulumukira kuti muthe kuwapirira.+

  • Yakobo 1:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Munthu akakhala pa mayesero asamanene kuti: “Mulungu akundiyesa.” Chifukwa Mulungu sangayesedwe ndi zinthu zoipa ndipo iye sayesa munthu ndi zinthu zoipa.

  • Chivumbulutso 3:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Chifukwa chakuti unasunga mawu onena za kupirira kwanga,*+ inenso ndidzakuteteza pa ola la kuyesedwa+ limene likubwera padziko lonse lapansi kumene kuli anthu. Ndidzakuteteza pa ola limene likubwera kudzayesa anthu amene akukhala padziko lapansi.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena