Luka 18:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 ndionetsetsa kuti chilungamo chachitika kwa mkazi wamasiyeyu chifukwa choti akundivutitsa. Ndichita zimenezi kuti asapitirize kubwera nʼkunditopetsa ndi zimene akupemphazo.’”+
5 ndionetsetsa kuti chilungamo chachitika kwa mkazi wamasiyeyu chifukwa choti akundivutitsa. Ndichita zimenezi kuti asapitirize kubwera nʼkunditopetsa ndi zimene akupemphazo.’”+