Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 24:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Koma amene adzapirire* mpaka pamapeto ndi amene adzapulumuke.+

  • Aroma 5:3, 4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Si zokhazo, koma tikhozanso kumasangalala* tikakumana ndi mavuto+ chifukwa tikudziwa kuti mavuto athu amachititsa kuti tipirire.+ 4 Kupirira kumachititsa kuti tikhale ovomerezeka kwa Mulungu+ ndipo kukhala ovomerezeka kwa Mulungu kumachititsa kuti tikhale ndi chiyembekezo.+

  • Aheberi 10:36
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 36 Mukufunika kukhala opirira+ komanso kuchita chifuniro cha Mulungu kuti mudzalandire zimene Mulunguyo walonjeza.

  • 2 Petulo 1:5, 6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Chifukwa cha zimenezi, yesetsani mwakhama+ kuwonjezera makhalidwe abwino+ pa chikhulupiriro chanu, pa makhalidwe anu abwino muwonjezerepo kudziwa zinthu,+ 6 pa kudziwa zinthu kudziletsa,+ pa kudziletsa kupirira, pa kupirira kudzipereka kwa Mulungu,+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena