Aheberi 10:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Tayeretsedwa ndi “chifuniro” chimenecho,+ kudzera mʼthupi la Yesu Khristu limene analipereka nsembe kamodzi kokha.+ 1 Petulo 2:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Iye ananyamula machimo athu+ mʼthupi lake pamene anamukhomerera pamtengo.+ Anachita zimenezi kuti tipulumutsidwe ku uchimo nʼkumachita zinthu zolungama. Ndipo “munachiritsidwa ndi mabala ake.”+
10 Tayeretsedwa ndi “chifuniro” chimenecho,+ kudzera mʼthupi la Yesu Khristu limene analipereka nsembe kamodzi kokha.+
24 Iye ananyamula machimo athu+ mʼthupi lake pamene anamukhomerera pamtengo.+ Anachita zimenezi kuti tipulumutsidwe ku uchimo nʼkumachita zinthu zolungama. Ndipo “munachiritsidwa ndi mabala ake.”+