Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 20:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Izi zikufanana ndi zimene Mwana wa munthu anachita. Iye sanabwere kudzatumikiridwa koma kudzatumikira+ ndi kudzapereka moyo wake dipo* kuti awombole anthu ambiri.”+

  • Yohane 13:3-5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Yesu ankadziwa kuti Atate anapereka zinthu zonse mʼmanja mwake komanso kuti anabwera kuchokera kwa Mulungu ndiponso kuti ankapita kwa Mulungu.+ 4 Choncho anaimirira pa chakudya chamadzulocho nʼkuvula malaya ake akunja. Kenako anatenga thaulo nʼkulimanga mʼchiuno mwake.+ 5 Atatero anathira madzi mʼbeseni nʼkuyamba kusambitsa mapazi a ophunzirawo komanso kuwapukuta ndi thaulo limene anamanga mʼchiuno lija.

  • Afilipi 2:5-7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Khalani ndi maganizo amenenso Khristu Yesu anali nawo.+ 6 Ngakhale kuti iye ankaoneka ngati Mulungu,+ sanaganizirepo zoti ayese kulanda udindo wa Mulungu kuti akhale wofanana naye.+ 7 Ayi sanachite zimenezo, koma anasiya zonse zimene anali nazo nʼkukhala ngati kapolo+ ndipo anakhala munthu.*+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena