Mateyu 27:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndipo atamumanga, anapita kukamupereka kwa Bwanamkubwa Pilato.+ Maliko 15:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mwamsanga mʼbandakucha, ansembe aakulu limodzi ndi akulu komanso alembi, kutanthauza Khoti lonse Lalikulu la Ayuda,* anasonkhana pamodzi kuti agwirizane zoti amuchite Yesu. Kenako anamumanga nʼkupita naye kukamupereka kwa Pilato.+ Yohane 18:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ndiyeno iwo anatenga Yesu kuchoka kwa Kayafa nʼkupita naye kunyumba ya bwanamkubwa.+ Umenewu unali mʼmawa kwambiri. Koma iwo sanalowe mʼnyumba ya bwanamkubwayo poopa kudetsedwa.+ Iwo ankafuna kuti akathe kudya Pasika.
15 Mwamsanga mʼbandakucha, ansembe aakulu limodzi ndi akulu komanso alembi, kutanthauza Khoti lonse Lalikulu la Ayuda,* anasonkhana pamodzi kuti agwirizane zoti amuchite Yesu. Kenako anamumanga nʼkupita naye kukamupereka kwa Pilato.+
28 Ndiyeno iwo anatenga Yesu kuchoka kwa Kayafa nʼkupita naye kunyumba ya bwanamkubwa.+ Umenewu unali mʼmawa kwambiri. Koma iwo sanalowe mʼnyumba ya bwanamkubwayo poopa kudetsedwa.+ Iwo ankafuna kuti akathe kudya Pasika.