Yohane 18:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Yesu anayankha kuti:+ “Ufumu wanga si wamʼdzikoli.+ Ufumu wanga ukanakhala wamʼdzikoli, atumiki anga akanamenya nkhondo kuti ndisaperekedwe kwa Ayuda.+ Koma Ufumu wanga si wochokera mʼdzikoli.”
36 Yesu anayankha kuti:+ “Ufumu wanga si wamʼdzikoli.+ Ufumu wanga ukanakhala wamʼdzikoli, atumiki anga akanamenya nkhondo kuti ndisaperekedwe kwa Ayuda.+ Koma Ufumu wanga si wochokera mʼdzikoli.”