Mateyu 27:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Nawonso achifwamba amene anapachikidwa naye limodzi ankamunyoza.+ Maliko 15:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Tsopanotu Khristu, Mfumu ya Isiraeli, itsike pamtengo wozunzikirapowo,* kuti ife tione ndi kukhulupirira.”+ Nawonso achifwamba amene anapachikidwa naye limodzi aja ankamunyoza.+
32 Tsopanotu Khristu, Mfumu ya Isiraeli, itsike pamtengo wozunzikirapowo,* kuti ife tione ndi kukhulupirira.”+ Nawonso achifwamba amene anapachikidwa naye limodzi aja ankamunyoza.+