Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Afilipi 2:9-11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Pa chifukwa chimenechi, Mulungu anamukweza nʼkumupatsa udindo wapamwamba+ ndipo mokoma mtima anamupatsa dzina loposa lina lililonse.+ 10 Anachita zimenezi kuti mʼdzina la Yesu, onse apinde mawondo awo, kaya ali kumwamba, padziko lapansi kapena pansi pa nthaka.*+ 11 Komanso kuti aliyense avomereze poyera kuti Yesu Khristu ndi Ambuye,+ zimene zidzapereka ulemerero kwa Mulungu Atate.

  • Aheberi 2:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Koma tikuona Yesu, amene anamutsitsa pangʼono poyerekeza ndi angelo.+ Panopa amuveka ulemerero ndi ulemu ngati chisoti chachifumu chifukwa chakuti anafa.+ Chifukwa cha kukoma mtima kwakukulu kwa Mulungu, zimenezi zinamuchitikira kuti alawe imfa mʼmalo mwa munthu aliyense.+

  • 1 Petulo 1:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Mzimu woyera unali utaneneratu kuti Khristu+ adzavutika ndipo kenako adzalandira ulemerero. Aneneri ankafufuza zizindikiro zimene mzimu woyera* unawasonyeza zokhudza nthawi yeniyeni komanso nyengo imene zimenezi zidzachitike.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena