Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 1:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Kenako Mulungu anati: “Tiyeni+ tipange munthu mʼchifaniziro+ chathu, kuti akhale wofanana nafe.+ Ayangʼanire nsomba zamʼnyanja, zamoyo zouluka mumlengalenga, nyama zoweta ndiponso nyama iliyonse yokwawa padziko lapansi. Komanso asamalire dziko lonse lapansi.”+

  • 1 Akorinto 8:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Koma kwa ife Mulungu alipo mmodzi yekha,+ amene ndi Atate.+ Zinthu zonse zinachokera kwa iye, ndipo ifeyo ndife ake.+ Palinso Ambuye mmodzi, Yesu Khristu, amene zinthu zonse zinakhalapo kudzera mwa iye,+ ndipo ifeyo kudzera mwa iyeyo.

  • Akolose 1:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Kudzera mwa iye, Mulungu analenga zinthu zina zonse kumwamba ndi padziko lapansi. Analenga zinthu zooneka ndi zinthu zosaoneka,+ kaya ndi mipando yachifumu, ambuye, maboma komanso maulamuliro. Inde, analenga zinthu zina zonse kudzera mwa iye+ ndiponso chifukwa cha iye.

  • Aheberi 1:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Kumapeto kwa masiku ano, iye walankhula ndi ife kudzera mwa Mwana wake,+ amene anamusankha kuti akhale wolandira zinthu zonse monga cholowa.+ Komanso kudzera mwa iyeyu, Mulungu anachititsa kuti pakhale nthawi* zosiyanasiyana.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena