Aroma 8:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Onse amene akutsogoleredwa ndi mzimu wa Mulungu, ndi anadi a Mulungu.+ Aroma 8:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mzimuwo umachitira umboni limodzi ndi mzimu wathu+ kuti ndife ana a Mulungu.+ 2 Akorinto 6:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “‘Ndidzakhala bambo anu+ ndipo inu mudzakhala ana anga aamuna ndi aakazi,’+ watero Yehova* Wamphamvuyonse.” Aefeso 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chifukwa anatisankhiratu+ kuti adzatitenga nʼkukhala ana ake+ kudzera mwa Yesu Khristu, mogwirizana ndi zimene zinamusangalatsa komanso zimene anafuna.+ 1 Yohane 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Taganizirani za chikondi chachikulu chimene Atate watisonyeza+ potitchula kuti ana ake.*+ Ndipo ndifedi ana ake. Nʼchifukwa chake dziko silikutidziwa,+ popeza iyeyo silikumudziwanso.+
18 “‘Ndidzakhala bambo anu+ ndipo inu mudzakhala ana anga aamuna ndi aakazi,’+ watero Yehova* Wamphamvuyonse.”
5 Chifukwa anatisankhiratu+ kuti adzatitenga nʼkukhala ana ake+ kudzera mwa Yesu Khristu, mogwirizana ndi zimene zinamusangalatsa komanso zimene anafuna.+
3 Taganizirani za chikondi chachikulu chimene Atate watisonyeza+ potitchula kuti ana ake.*+ Ndipo ndifedi ana ake. Nʼchifukwa chake dziko silikutidziwa,+ popeza iyeyo silikumudziwanso.+