Mateyu 14:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Atauza anthuwo kuti azipita, anakwera phiri yekhayekha kukapemphera.+ Iye anakhala kumeneko yekhayekha mpaka kunja kunada. Maliko 6:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Kenako mwamsanga, Yesu anauza ophunzira ake kuti akwere ngalawa nʼkutsogola kupita kutsidya lina loyangʼanizana nalo cha ku Betsaida. Koma iye anatsalira nʼcholinga choti auze anthuwo kuti azipita kwawo.+
23 Atauza anthuwo kuti azipita, anakwera phiri yekhayekha kukapemphera.+ Iye anakhala kumeneko yekhayekha mpaka kunja kunada.
45 Kenako mwamsanga, Yesu anauza ophunzira ake kuti akwere ngalawa nʼkutsogola kupita kutsidya lina loyangʼanizana nalo cha ku Betsaida. Koma iye anatsalira nʼcholinga choti auze anthuwo kuti azipita kwawo.+