Mateyu 26:14, 15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kenako mmodzi wa ophunzira 12 aja, amene ankadziwika kuti Yudasi Isikariyoti,+ anapita kwa ansembe aakulu+ 15 nʼkuwafunsa kuti: “Kodi mudzandipatsa chiyani ndikamupereka kwa inu?”+ Iwo anamulonjeza ndalama 30 zasiliva.+ Yohane 12:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma Yudasi Isikariyoti,+ mmodzi wa ophunzira ake, amene anali atatsala pangʼono kumupereka anati:
14 Kenako mmodzi wa ophunzira 12 aja, amene ankadziwika kuti Yudasi Isikariyoti,+ anapita kwa ansembe aakulu+ 15 nʼkuwafunsa kuti: “Kodi mudzandipatsa chiyani ndikamupereka kwa inu?”+ Iwo anamulonjeza ndalama 30 zasiliva.+