Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 26:47
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 47 Mawu adakali mʼkamwa, Yudasi, mmodzi wa ophunzira 12 aja, anafika limodzi ndi gulu lalikulu la anthu kuchokera kwa ansembe aakulu ndi kwa akulu, atanyamula malupanga ndi zibonga.+

  • Maliko 14:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Kenako Yudasi Isikariyoti, mmodzi wa ophunzira 12 aja, anachoka nʼkupita kwa ansembe aakulu kuti akapereke Yesu kwa iwo.+

  • Luka 22:48
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 48 Koma Yesu anamufunsa kuti: “Yudasi, kodi ukupereka Mwana wa munthu ndi kisi?”

  • Yohane 13:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Popeza Yudasi ankasunga bokosi la ndalama,+ ena ankaganiza kuti Yesu ankamuuza kuti, “Ugule zinthu zonse zimene zikufunikira pachikondwerero,” kapena kuti apereke kenakake kwa osauka.

  • Machitidwe 1:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 “Abale anga, zinali zofunika kuti lemba likwaniritsidwe, limene mzimu woyera unaneneratu kudzera mwa Davide. Lembali ndi lokhudza Yudasi,+ amene anatsogolera anthu okagwira Yesu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena