Luka 3:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Tsopano anthu ankayembekezera Khristu ndipo onse ankaganiza mʼmitima yawo za Yohane kuti, “Kodi Khristu uja si ameneyu?”+
15 Tsopano anthu ankayembekezera Khristu ndipo onse ankaganiza mʼmitima yawo za Yohane kuti, “Kodi Khristu uja si ameneyu?”+