Yohane 10:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Koma ngati ndikuzichita, ngakhale simukundikhulupirira, khulupirirani ntchitozo,+ kuti mudziwe ndi kupitirizabe kudziwa kuti Atate ndi ine ndife ogwirizana.”+ Yohane 17:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ine sindipitiriza kukhala mʼdzikoli chifukwa ndikubwera kwa inu, koma iwowo adakali mʼdzikoli.+ Atate Woyera, ayangʼanireni+ chifukwa cha dzina lanu limene mwandipatsa, kuti akhale amodzi* ngati mmene ife tilili.+ Yohane 17:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndikuchita zimenezi kuti onsewa akhale amodzi+ ngati mmene inu Atate ndi ine tilili ogwirizana,+ kuti iwonso akhale ogwirizana ndi ife nʼcholinga choti dziko likhulupirire kuti inu munanditumadi.
38 Koma ngati ndikuzichita, ngakhale simukundikhulupirira, khulupirirani ntchitozo,+ kuti mudziwe ndi kupitirizabe kudziwa kuti Atate ndi ine ndife ogwirizana.”+
11 Ine sindipitiriza kukhala mʼdzikoli chifukwa ndikubwera kwa inu, koma iwowo adakali mʼdzikoli.+ Atate Woyera, ayangʼanireni+ chifukwa cha dzina lanu limene mwandipatsa, kuti akhale amodzi* ngati mmene ife tilili.+
21 Ndikuchita zimenezi kuti onsewa akhale amodzi+ ngati mmene inu Atate ndi ine tilili ogwirizana,+ kuti iwonso akhale ogwirizana ndi ife nʼcholinga choti dziko likhulupirire kuti inu munanditumadi.