-
Luka 19:37Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
37 Atangofika pafupi ndi msewu wochokera mʼphiri la Maolivi, gulu lonse la ophunzirawo linayamba kusangalala ndi kutamanda Mulungu mokweza mawu chifukwa cha ntchito zonse zamphamvu zimene anaona.
-