Genesis 28:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Yakobo anachoka ku Beere-seba nʼkupitiriza ulendo wake wopita ku Harana.+ Genesis 28:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kenako anayamba kulota. Mʼmalotowo anaona masitepe* ochokera padziko lapansi mpaka kumwamba, angelo a Mulungu akukwera ndi kutsika pamasitepewo.+ Salimo 104:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iye amachititsa kuti angelo ake akhale amphamvu,*Amachititsa atumiki ake kuti akhale moto wopsereza.+ Danieli 7:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndinapitiriza kuona masomphenya usikuwo ndipo ndinaona winawake wooneka ngati mwana wa munthu+ akubwera mʼmitambo. Iye analoledwa kufika kwa Wamasiku Ambiri+ uja ndipo anamubweretsa pafupi kwambiri ndi Wamasiku Ambiriyo. Mateyu 4:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kenako Mdyerekezi uja anamusiya+ ndipo kunabwera angelo nʼkuyamba kumutumikira.+ Luka 22:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Atatero mngelo wochokera kumwamba anaonekera kwa iye nʼkumulimbikitsa.+
12 Kenako anayamba kulota. Mʼmalotowo anaona masitepe* ochokera padziko lapansi mpaka kumwamba, angelo a Mulungu akukwera ndi kutsika pamasitepewo.+
4 Iye amachititsa kuti angelo ake akhale amphamvu,*Amachititsa atumiki ake kuti akhale moto wopsereza.+
13 Ndinapitiriza kuona masomphenya usikuwo ndipo ndinaona winawake wooneka ngati mwana wa munthu+ akubwera mʼmitambo. Iye analoledwa kufika kwa Wamasiku Ambiri+ uja ndipo anamubweretsa pafupi kwambiri ndi Wamasiku Ambiriyo.