-
Luka 22:39-41Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
39 Atachoka kumeneko anapita kuphiri la Maolivi ngati mmene ankachitira nthawi zonse ndipo ophunzira ake nawonso anamutsatira.+ 40 Atafika pamalowo anauza ophunzirawo kuti: “Pitirizani kupemphera kuti musalowe mʼmayesero.”+ 41 Iye anachoka pamene panali ophunzirawo nʼkuyenda kamtunda, kutalika kwake ngati pamene pangagwere mwala munthu atauponya. Kumeneko anagwada nʼkuyamba kupemphera
-