-
Luka 4:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Komanso anayamba kuphunzitsa mʼmasunagoge awo ndipo anthu onse ankamulemekeza.
-
-
Yohane 7:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Chikondwererocho chitafika pakatikati, Yesu analowa mʼkachisi ndipo anayamba kuphunzitsa.
-