Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 20:18, 19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 “Tsopano tikupita ku Yerusalemu ndipo Mwana wa munthu akaperekedwa kwa ansembe aakulu ndi alembi. Iwo akamuweruza kuti aphedwe+ 19 ndipo akamupereka kwa anthu a mitundu ina kuti amuchitire chipongwe, kumukwapula ndi kumupachika pamtengo+ ndipo pa tsiku lachitatu adzaukitsidwa.”+

  • Yohane 3:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Mofanana ndi Mose amene anakweza njoka mʼmwamba mʼchipululu,+ Mwana wa munthunso akuyenera kukwezedwa mʼmwamba+

  • Yohane 12:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Koma ine ndikadzakwezedwa mʼmwamba padziko lapansi,+ ndidzakokera anthu osiyanasiyana kwa ine.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena