-
Genesis 21:1-3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Yehova anakumbukira Sara monga mmene ananenera, ndipo Yehova anachitira Sara mogwirizana ndi zimene analonjeza.+ 2 Choncho Sara anakhala woyembekezera+ ndipo anaberekera Abulahamu mwana, Abulahamuyo atakalamba. Izi zinachitika ndendende pa nthawi imene Mulungu analonjeza Abulahamu.+ 3 Abulahamu anapatsa mwana amene Sara anamuberekerayo dzina lakuti Isaki.+
-