Mateyu 10:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Ndiponso aliyense amene sakufuna kunyamula mtengo wake wozunzikirapo* nʼkupitiriza kunditsatira ndi wosayenera kuti akhale wophunzira wanga.+ Yohane 15:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mukanakhala mbali ya dziko, dziko likanakukondani monga mbali yake. Popeza simuli mbali ya dzikoli,+ koma ine ndinakusankhani kuchokera mʼdziko, pa chifukwa chimenechi dziko likudana nanu.+ Aroma 8:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Choncho ngati tili ana, ndifenso olandira cholowa kuchokera kwa Mulungu. Koma ndifenso olandira cholowa+ anzake a Khristu, ngati tikuvutika naye limodzi+ kuti tikalandire naye ulemerero.+ 1 Atesalonika 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Chifukwa pamene tinali nanu limodzi, tinkakuuziranitu kuti tidzakumana ndi mavuto ndipo monga mmene mukudziwira, zimene tinkakuuzanizo ndi zimene zachitikadi.+
38 Ndiponso aliyense amene sakufuna kunyamula mtengo wake wozunzikirapo* nʼkupitiriza kunditsatira ndi wosayenera kuti akhale wophunzira wanga.+
19 Mukanakhala mbali ya dziko, dziko likanakukondani monga mbali yake. Popeza simuli mbali ya dzikoli,+ koma ine ndinakusankhani kuchokera mʼdziko, pa chifukwa chimenechi dziko likudana nanu.+
17 Choncho ngati tili ana, ndifenso olandira cholowa kuchokera kwa Mulungu. Koma ndifenso olandira cholowa+ anzake a Khristu, ngati tikuvutika naye limodzi+ kuti tikalandire naye ulemerero.+
4 Chifukwa pamene tinali nanu limodzi, tinkakuuziranitu kuti tidzakumana ndi mavuto ndipo monga mmene mukudziwira, zimene tinkakuuzanizo ndi zimene zachitikadi.+