-
2 Petulo 1:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
1 Ndine Simoni Petulo, kapolo komanso mtumwi wa Yesu Khristu. Ndikulembera anthu amene apeza chikhulupiriro chamtengo wapatali chofanana ndi chathu kudzera mʼchilungamo cha Mulungu wathu ndiponso cha Mpulumutsi wathu Yesu Khristu.
-