Aefeso 6:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Tsopano, kuti mudziwenso mmene zinthu zikuyendera pa moyo wanga ndi mmene ine ndilili, Tukiko,+ mʼbale wokondedwa ndiponso mtumiki wokhulupirika wa Ambuye, adzakufotokozerani zonse.+ Akolose 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Tukiko+ amene ndi mʼbale wanga wokondedwa, mtumiki wokhulupirika komanso kapolo mnzanga mwa Ambuye, adzakuuzani zonse zokhudza ine. 2 Timoteyo 4:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Koma Tukiko+ ndamutuma ku Efeso.
21 Tsopano, kuti mudziwenso mmene zinthu zikuyendera pa moyo wanga ndi mmene ine ndilili, Tukiko,+ mʼbale wokondedwa ndiponso mtumiki wokhulupirika wa Ambuye, adzakufotokozerani zonse.+
7 Tukiko+ amene ndi mʼbale wanga wokondedwa, mtumiki wokhulupirika komanso kapolo mnzanga mwa Ambuye, adzakuuzani zonse zokhudza ine.