Genesis 15:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Abulamu anakhulupirira zimene Yehova anamuuza,+ ndipo Mulunguyo anamuona kuti ndi wolungama.+ Yakobo 2:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Choncho lemba linakwaniritsidwa limene limati: “Abulahamu anakhulupirira zimene Yehova* anamuuza ndipo ankaonedwa kuti ndi wolungama,”+ choncho ankadziwika kuti ndi mnzake wa Yehova.*+
23 Choncho lemba linakwaniritsidwa limene limati: “Abulahamu anakhulupirira zimene Yehova* anamuuza ndipo ankaonedwa kuti ndi wolungama,”+ choncho ankadziwika kuti ndi mnzake wa Yehova.*+