Salimo 51:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Taonani! Ndinabadwa ndili wochimwa,Ndipo ndine wochimwa kuchokera pamene mayi anga anatenga pakati panga.+ Yohane 8:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Yesu anawayankha kuti: “Ndithudi ndikukuuzani, aliyense amene akuchita tchimo ndi kapolo wa tchimo.+ Aroma 6:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kodi simukudziwa kuti mukamadzipereka kwa winawake ngati akapolo omvera, mumakhala akapolo a amene mukumumverayo?+ Mumakhala akapolo a uchimo+ umene umatsogolera ku imfa,+ kapena akapolo a kumvera komwe kumatsogolera ku chilungamo.
5 Taonani! Ndinabadwa ndili wochimwa,Ndipo ndine wochimwa kuchokera pamene mayi anga anatenga pakati panga.+
34 Yesu anawayankha kuti: “Ndithudi ndikukuuzani, aliyense amene akuchita tchimo ndi kapolo wa tchimo.+
16 Kodi simukudziwa kuti mukamadzipereka kwa winawake ngati akapolo omvera, mumakhala akapolo a amene mukumumverayo?+ Mumakhala akapolo a uchimo+ umene umatsogolera ku imfa,+ kapena akapolo a kumvera komwe kumatsogolera ku chilungamo.