1 Yohane 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Okondedwa, tsopano ndife ana a Mulungu,+ koma panopa sizinaonekerebe kuti tidzakhala otani.+ Tikudziwa kuti akadzaonekera, tidzakhala ngati iyeyo, chifukwa tidzamuona mmene alili.
2 Okondedwa, tsopano ndife ana a Mulungu,+ koma panopa sizinaonekerebe kuti tidzakhala otani.+ Tikudziwa kuti akadzaonekera, tidzakhala ngati iyeyo, chifukwa tidzamuona mmene alili.