Aroma 5:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Choncho, mmene zinakhalira kuti uchimo umodzi unachititsa kuti anthu osiyanasiyana aweruzidwe kuti ndi ochimwa,+ kuchita chinthu chimodzi cholungama kwachititsanso kuti anthu osiyanasiyana+ aonedwe kuti ndi olungama kuti akhale ndi moyo.+ Tito 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 kuti titayesedwa olungama chifukwa cha kukoma mtima kwake kwakukulu,+ tingakhale olandira cholowa+ mogwirizana ndi chiyembekezo cha moyo wosatha.+
18 Choncho, mmene zinakhalira kuti uchimo umodzi unachititsa kuti anthu osiyanasiyana aweruzidwe kuti ndi ochimwa,+ kuchita chinthu chimodzi cholungama kwachititsanso kuti anthu osiyanasiyana+ aonedwe kuti ndi olungama kuti akhale ndi moyo.+
7 kuti titayesedwa olungama chifukwa cha kukoma mtima kwake kwakukulu,+ tingakhale olandira cholowa+ mogwirizana ndi chiyembekezo cha moyo wosatha.+