Aroma 6:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Koma tsopano chifukwa munamasulidwa ku uchimo nʼkukhala akapolo a Mulungu, mukubala zipatso za chiyero+ ndipo pamapeto pake mudzakhala ndi moyo wosatha.+
22 Koma tsopano chifukwa munamasulidwa ku uchimo nʼkukhala akapolo a Mulungu, mukubala zipatso za chiyero+ ndipo pamapeto pake mudzakhala ndi moyo wosatha.+