-
1 Akorinto 8:10, 11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Ngati wina angaone iweyo wodziwa zinthuwe ukudya chakudya mʼkachisi wa mafano, kodi chikumbumtima cha munthu wofookayo sichidzamulimbikitsa kudya zakudya zoperekedwa kwa mafano? 11 Choncho kudziwa zinthu kwako kungachititse kuti uwononge munthu wofookayo, yemwe ndi mʼbale wako amene Khristu anamufera.+
-