1 Akorinto 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Tsopano ndikukudandaulirani abale, mʼdzina la Ambuye wathu Yesu Khristu, kuti nonse muzilankhula mogwirizana ndipo pakati panu pasakhale kugawanika,+ koma mukhale ogwirizana kwambiri pokhala ndi mtima umodzi ndi maganizo amodzi.+ 2 Akorinto 13:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pomaliza abale, pitirizani kusangalala, kusintha maganizo, kulimbikitsidwa,+ kukhala ndi maganizo ogwirizana+ ndiponso kukhala mwamtendere.+ Mukatero, Mulungu amene ndi wachikondi komanso wamtendere+ adzakhala nanu. Afilipi 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mukamachita zimenezi, mudzachititsa kuti chimwemwe changa chisefukire. Muzisonyeza kuti mumaganiza mofanana, muli ndi chikondi chofanana komanso kuti ndinu ogwirizana kwambiri ndipo maganizo anu ndi amodzi.+ 1 Petulo 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pomaliza, nonsenu mukhale amaganizo amodzi,+ muzimverana chisoni, muzikonda abale, mukhale ndi chifundo chachikulu+ ndiponso mukhale odzichepetsa.+
10 Tsopano ndikukudandaulirani abale, mʼdzina la Ambuye wathu Yesu Khristu, kuti nonse muzilankhula mogwirizana ndipo pakati panu pasakhale kugawanika,+ koma mukhale ogwirizana kwambiri pokhala ndi mtima umodzi ndi maganizo amodzi.+
11 Pomaliza abale, pitirizani kusangalala, kusintha maganizo, kulimbikitsidwa,+ kukhala ndi maganizo ogwirizana+ ndiponso kukhala mwamtendere.+ Mukatero, Mulungu amene ndi wachikondi komanso wamtendere+ adzakhala nanu.
2 Mukamachita zimenezi, mudzachititsa kuti chimwemwe changa chisefukire. Muzisonyeza kuti mumaganiza mofanana, muli ndi chikondi chofanana komanso kuti ndinu ogwirizana kwambiri ndipo maganizo anu ndi amodzi.+
8 Pomaliza, nonsenu mukhale amaganizo amodzi,+ muzimverana chisoni, muzikonda abale, mukhale ndi chifundo chachikulu+ ndiponso mukhale odzichepetsa.+