Mateyu 18:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Amenewanso akapanda kuwamvera, uuze mpingo. Ndipo mpingowo akapandanso kuumvera, kwa iwe akhale ngati munthu wochokera kumtundu wina+ komanso ngati wokhometsa msonkho.+
17 Amenewanso akapanda kuwamvera, uuze mpingo. Ndipo mpingowo akapandanso kuumvera, kwa iwe akhale ngati munthu wochokera kumtundu wina+ komanso ngati wokhometsa msonkho.+