Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Aroma 12:4, 5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Thupi limakhala ndi ziwalo zambiri,+ koma ziwalozo sizigwira ntchito yofanana. 5 Chimodzimodzinso ifeyo, ngakhale kuti tilipo ambiri, ndife thupi limodzi mwa Khristu ndipo ndife ziwalo zolumikizana.+

  • 1 Akorinto 12:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Koma Mulungu anaika ziwalo zonse za thupi, chilichonse pamalo ake, mmene iye anafunira.

  • 1 Akorinto 12:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Ndinu thupi la Khristu+ ndipo aliyense wa inu ndi chiwalo cha thupilo.+

  • Aefeso 4:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Koma tizilankhula zoona ndiponso kusonyeza chikondi. Tikatero tidzakhala achikulire mʼzinthu zonse ndipo tidzatha kuchita zinthu mogwirizana ndi Khristu, amene ndi mutu.+

  • Aefeso 5:29, 30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 chifukwa palibe munthu amene anadanapo ndi thupi lake, koma amalidyetsa ndi kulikonda, ngati mmene Khristu amachitira ndi mpingo 30 chifukwa ndife ziwalo za thupi lake.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena