Mateyu 18:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma aliyense wokhumudwitsa mmodzi wa tiana iti timene timandikhulupirira, zingamukhalire bwino kwambiri kumumangirira chimwala cha mphero mʼkhosi mwake chimene bulu amayendetsa, nʼkumuponyera mʼnyanja yakuya.+ Aroma 14:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Chifukwa ngati mʼbale wanu akukhumudwa chifukwa cha chakudya, ndiye kuti simukusonyezanso chikondi.+ Musawononge* munthu amene Khristu anamufera chifukwa cha zakudya zanu.+ Aroma 14:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndi bwino kusadya nyama kapena kusamwa vinyo kapena kusachita chilichonse chimene chimakhumudwitsa mʼbale wako.+
6 Koma aliyense wokhumudwitsa mmodzi wa tiana iti timene timandikhulupirira, zingamukhalire bwino kwambiri kumumangirira chimwala cha mphero mʼkhosi mwake chimene bulu amayendetsa, nʼkumuponyera mʼnyanja yakuya.+
15 Chifukwa ngati mʼbale wanu akukhumudwa chifukwa cha chakudya, ndiye kuti simukusonyezanso chikondi.+ Musawononge* munthu amene Khristu anamufera chifukwa cha zakudya zanu.+
21 Ndi bwino kusadya nyama kapena kusamwa vinyo kapena kusachita chilichonse chimene chimakhumudwitsa mʼbale wako.+