Aroma 8:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Koma ngati zimene tikuyembekezera+ sizinachitike,+ timadikirabe mopirira.+ Aroma 12:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kondwerani chifukwa cha chiyembekezo. Muzipirira mavuto.+ Muzilimbikira kupemphera.+