Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Aroma 5:3-5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Si zokhazo, koma tikhozanso kumasangalala* tikakumana ndi mavuto+ chifukwa tikudziwa kuti mavuto athu amachititsa kuti tipirire.+ 4 Kupirira kumachititsa kuti tikhale ovomerezeka kwa Mulungu+ ndipo kukhala ovomerezeka kwa Mulungu kumachititsa kuti tikhale ndi chiyembekezo.+ 5 Chiyembekezocho sichitikhumudwitsa+ chifukwa Mulungu amasonyeza kuti amatikonda pogwiritsa ntchito mzimu woyera umene amatipatsa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena