Yesaya 53:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Anapatsidwa manda* limodzi ndi anthu oipa,+Ndipo pamene anafa anaikidwa mʼmanda limodzi ndi anthu olemera,*+Ngakhale kuti iye sanalakwe chilichonse*Ndipo mʼkamwa mwake munalibe chinyengo.+ Mateyu 27:59, 60 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 59 Yosefe anatenga mtembowo nʼkuukulunga munsalu yoyera yabwino kwambiri,+ 60 ndipo anakauika mʼmanda*+ ake atsopano amene anawasema muthanthwe. Kenako atagubuduza chimwala chachikulu nʼkutseka pakhomo la mandawo,* anachoka.
9 Anapatsidwa manda* limodzi ndi anthu oipa,+Ndipo pamene anafa anaikidwa mʼmanda limodzi ndi anthu olemera,*+Ngakhale kuti iye sanalakwe chilichonse*Ndipo mʼkamwa mwake munalibe chinyengo.+
59 Yosefe anatenga mtembowo nʼkuukulunga munsalu yoyera yabwino kwambiri,+ 60 ndipo anakauika mʼmanda*+ ake atsopano amene anawasema muthanthwe. Kenako atagubuduza chimwala chachikulu nʼkutseka pakhomo la mandawo,* anachoka.