19 Tsopano ntchito za thupi lochimwali zimaonekera mosavuta. Ntchito zimenezi ndi chiwerewere,+ khalidwe limene limadetsa munthu, khalidwe lopanda manyazi,+ 20 kulambira mafano, kukhulupirira mizimu,+ chidani, ndewu, nsanje, kupsa mtima, mikangano, kugawikana, magulu ampatuko,