Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 13:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Koma iye anawayankha kuti: “Inu mwapatsidwa mwayi woti mumvetse zinsinsi zopatulika+ za Ufumu wakumwamba, koma anthu amenewa sanapatsidwe mwayi umenewo.

  • Aroma 16:25, 26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Mulungu angakulimbitseni pogwiritsa ntchito uthenga wabwino umene ndikulengeza ndiponso uthenga wonena za Yesu Khristu umene ukulalikidwa. Uthengawu ndi wogwirizana ndi zimene zaululidwa zokhudza chinsinsi chopatulika+ chimene chakhala chobisika kwa nthawi yaitali. 26 Koma tsopano chinsinsi chimenechi chaululidwa ndipo anthu a mitundu yonse achidziwa kudzera mʼMalemba aulosi. Zimenezi nʼzogwirizana ndi lamulo la Mulungu wamuyaya. Cholinga chake nʼchakuti anthu a mitundu yonse azimumvera mwa chikhulupiriro.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena