-
Yakobo 4:1, 2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Kodi nkhondo ndi ndewu zimene zikuchitika pakati panu zikuchokera kuti? Kodi sizikuchokera mʼzilakolako za thupi lanu zimene zikulimbana kuti zizilamulira matupi anu?*+ 2 Mumalakalaka, koma simulandira zimene mukulakalakazo. Mukupitiriza kupha anthu ndiponso mumasirira mwansanje koma simupeza kanthu. Mukupitiriza kukangana komanso kuchita nkhondo.+ Simunalandire chifukwa chakuti simunapemphe.
-