Aroma 8:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chifukwa otsatira zofuna za thupi, maganizo awo onse amakhala pa zinthu za thupi.+ Koma otsatira mzimu, maganizo awo onse amakhala pa zinthu za mzimu.+ Aroma 8:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Chifukwa ngati mukukhala motsatira zofuna za thupi, ndiye kuti mosakayikira mudzafa.+ Koma mukalola kuti mphamvu ya mzimu ikuthandizeni kupha zochita za thupi, mudzakhala ndi moyo.+
5 Chifukwa otsatira zofuna za thupi, maganizo awo onse amakhala pa zinthu za thupi.+ Koma otsatira mzimu, maganizo awo onse amakhala pa zinthu za mzimu.+
13 Chifukwa ngati mukukhala motsatira zofuna za thupi, ndiye kuti mosakayikira mudzafa.+ Koma mukalola kuti mphamvu ya mzimu ikuthandizeni kupha zochita za thupi, mudzakhala ndi moyo.+