Yakobo 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Paja tonsefe timapunthwa* nthawi zambiri.+ Ngati munthu sapunthwa pa mawu, ndiye kuti ndi wangwiro ndipo akhoza kulamuliranso thupi lake lonse.
2 Paja tonsefe timapunthwa* nthawi zambiri.+ Ngati munthu sapunthwa pa mawu, ndiye kuti ndi wangwiro ndipo akhoza kulamuliranso thupi lake lonse.