2 Petulo 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndipotu Mulungu sanalekerere angelo amene anachimwa aja+ osawapatsa chilango. Koma anawaponya mu Tatalasi,*+ anawamanga mumdima wandiweyani podikira kuti adzawaweruze.+
4 Ndipotu Mulungu sanalekerere angelo amene anachimwa aja+ osawapatsa chilango. Koma anawaponya mu Tatalasi,*+ anawamanga mumdima wandiweyani podikira kuti adzawaweruze.+