1 Akorinto 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Anthu azitha kuona kuti ndife atumiki a Khristu ndiponso atumiki a zinsinsi zopatulika za Mulungu.+ Aefeso 6:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Muzindipemphereranso ineyo kuti ndikayamba kulankhula ndizipeza mawu oyenerera nʼcholinga choti ndizitha kulankhula molimba mtima ndikamalalikira zokhudza chinsinsi chopatulika cha uthenga wabwino,+
4 Anthu azitha kuona kuti ndife atumiki a Khristu ndiponso atumiki a zinsinsi zopatulika za Mulungu.+
19 Muzindipemphereranso ineyo kuti ndikayamba kulankhula ndizipeza mawu oyenerera nʼcholinga choti ndizitha kulankhula molimba mtima ndikamalalikira zokhudza chinsinsi chopatulika cha uthenga wabwino,+