-
Aheberi 4:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Chifukwa mawu a Mulungu ndi amoyo komanso amphamvu,+ ndipo ndi akuthwa kuposa lupanga lililonse lakuthwa konsekonse.+ Amalasa munthu mumtima mpaka kulekanitsa moyo ndi mzimu komanso mafupa* ndi mafuta amʼmafupa. Mawu a Mulungu amathanso kuzindikira zimene munthu akuganiza komanso zolinga za mtima wake.
-